2 Mbiri 31

Afafaniza cipembedzo conse ca mafano 1 Citatha ici conse tsono, Aisrayeli onse opezekako anaturuka kumka ku midzi ya Yuda, naphwanya zoimiritsa, nalikha zifanizo, nagamula misanje ndi maguwa a nsembe m’Yuda…

2 Mbiri 32

Sanakeribu agwera Yuda 1 Zitatha zinthu izi zokhulupirika, anadza Sanakeribu mfumu ya Asuri, nalowera Yuda, namangira midzi yamalinga misasa, nati adzigonjetsere iyi. 2 Ndipo pakuona Hezekiya kuti wadza Sanakeribu, ndi…

2 Mbiri 33

Manase aikanso cipembedza ca mafano 1 Manase anali wa zaka khumi ndi ziwiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m’Yerusalemu zaka makumi asanu mphambu zisanu. 2 Nacita coipa pamaso pa Yehova,…

2 Mbiri 34

Yosiya acotsa cipembedzo ca mafano, nakonzanso Kacisi 1 Yosiya ndiye wa zaka zisanu ndi zitatu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m’Yerusalemu zaka makumi atatu mphambu cimodzi. 2 Nacita zoongoka pamaso…

2 Mbiri 35

Yosiya acita Paskha ku Yerusalemu 1 Pamenepo Yosiya anacitira Yehova Paskha m’Yerusalemu, naphera Paskha tsiku lakhumi ndi cinai la mwezi woyamba. 2 Ndipo anaika ansembe pa udikiro wao, nawalimbikitsa acite…

2 Mbiri 36

Yehoahazi, Yehoyakimu, Yehoyakini, mafumu a Yuda 1 Pamenepo anthu a m’dziko anatenga Yehoahazi mwana wa Yosiya, namlonga ufumu m’Yerusalemu, m’malo mwa atate wace. 2 Yehoahazi anali wa zaka makumi awiri…