2 Mbiri 21
Yoramu mfumu yoipitsitsa ya Yuda 1 Ndipo Yehosafati anagona pamodzi ndi makolo ace, naikidwa pamodzi ndi makolo ace m’mudzi wa Davide; ndi Yehoramu mwana wace anakhala mfumu m’malo mwace. 2…
Yoramu mfumu yoipitsitsa ya Yuda 1 Ndipo Yehosafati anagona pamodzi ndi makolo ace, naikidwa pamodzi ndi makolo ace m’mudzi wa Davide; ndi Yehoramu mwana wace anakhala mfumu m’malo mwace. 2…
Ahaziya mfumu ya Yuda aphedwa ndi Yehu 1 Ndipo okhala m’Yerusalemu anamlonga Ahaziya mwana wace wamng’ono akhale mfumu m’malo mwace; pakuti gulu la anthu, adadzawo pamodzi ndi Aarabu kucigono, adapha…
Yehoyada adzoza Yoasi akhale mfumu 1 Koma caka cacisanu ndi ciwiri Yehoyada anadzilimbitsa natenga atsogoleri a mazana, Azariya mwana wa Yeroamu, ndi Ismayeli mwana wa Yohanana, ndi Azariya mwana wa…
Yoasi akonzanso Kacisi 1 Yoasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m’Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la mace ndiye Zibiya wa ku Beereseba. 2…
Amaziya agonjetsa Aedomu 1 Amaziya anali wa zaka makumi awiri mphambu zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m’Yerusalemu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai; ndi dzina la mace ndiye…
Uziyaagonjetsa adani ambiri 1 Ndipo anthu onse Ayuda anatenga Uziya, ndiye wa zaka khumi mphambu zisanu ndi cimodzi, namlonga ufumu m’malo mwa atate wace Amaziya. 2 Iye anamanga Eloti, naubweza…
Yotamu mfumu ya Yuda 1 Yotamu anali wa zaka makumi awiri, mphambu zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m’Yerusalemu zaka khumi ndi zisanu ndi cimodzi; ndi dzina la mace ndiye…
Ahazi mfumu yoipitsitsa ya Yuda 1 Ahazi anali wa zaka makumi awiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m’Yerusalemu zaka khumi mphambu zisanu ndi cimodzi; koma sanacita zoongoka pamaso pa Yehova…
Hezekiya mfumu ya Yuda 1 Hezekiya analowa ufumu wace ali wa zaka makumi awiri mphambu zisanu, nakhala mfumu m’Yerusalemu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai; ndi dzina la mace…
Hezekiya acita Paskha ku Yerusalemu 1 Ndipo Hezekiya anatumiza kwa Israyeli ndi Yuda onse, nalembanso akalata kwa Efraimu ndi Manase, kuti abwere ku nyumba ya Yehova ku Yerusalemu, kucitira Yehova…