2 Mbiri 1

Solomo apereka nsembe ku Gibeoni 1 NDIPO Solomo mwana wa Davide analimbikitsidwa m’ufumu wace, ndipo Yehova Mulungu wace anali naye, namkuza kwakukuru. 2 Ndipo Solomo analankhula ndi Aisrayeli onse, ndi…

2 Mbiri 2

Solomo apangana ndi Hiramu za mirimo ya Kacisi 1 Ndipo a Solomo anati alimangire dzina la Yehova nyumba, ndiponso nyumba ya ufumu wace. 2 Nawerenga Solomo amuna zikwi khumi mphambu…

2 Mbiri 3

Mamangidwe a Kacisi 1 Pamenepo Solomo anayamba kumanga nyumba ya Yehova ku Yerusalemu, m’phiri la Moriya, kumene Mulungu anaonekera kwa Davide atate wace, pamalo pamene Davide anakonzeratu pa dwale la…

2 Mbiri 4

Guwa la nsembe ndi thawale lamkawa ndi zipangizo zonse zina 1 Anapanganso guwa la nsembe lamkuwa, m’litali mwace mikono makumi awiri, ndi kupingasa kwace mikono makumi awiri, ndi msinkhu wace…

2 Mbiri 5

1 Momwemo zidatha nchito zonse Solomo adazicitira nyumba ya Yehova. Ndipo Solomo anabwera nazo zopatulika zija za atate wace Davide; naziika siliva, ndi golidi, ndi zipangizo zonse m’cuma ca nyumba…

2 Mbiri 6

Conena Solomo ndi pemphero lace popereka Kacisi 1 Pamenepo Solomo anati, Yehova anati kuti adzakhala mu mdima wandiweyani. 2 Koma ndakumangirani nyumba yokhalamo, malo okhazikika okhalamo Inu nthawi yosatha. 3…

2 Mbiri 7

Cibvomerezo ca Yehova mwa moto ndi ulemerero wao wodzaza Kacisi 1 Atatha tsono Solomo kupemphera, moto unatsika kumwamba, nunyeketsa nsembe yopsereza, ndi nsembe zophera; ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza nyumbayi….

2 Mbiri 8

Solomo amanga midzi yina 1 Ndipo kunali, zitatha zaka makumi awiri m’mene anamanga nyumba ya Yehova, ndi nyumba yace yace, 2 Solomo anamanga midzi imene Huramu adampatsa, nakhalitsamo ana a…

2 Mbiri 9

Mfumu yaikazi ya ku Seba aceza ndi Solomo 1 Ndipo atamva mfumu yaikazi ya ku Seba mbiri ya Solomo, anadza kumuyesera Solomo ndi miyambi yododometsa ku Yerusalemu, ndi ulendo waukuru,…

2 Mbiri 10

Ufumu ugawanika pakati. Rehabiamu mfumu ya Yuda, Yerobiamu ya Israyeli 1 Ndipo Rehabiamu anamuka ku Sekemu; pakuti Aisrayeli onse adadza ku Sekemu kumlonga ufumu. 2 Ndipo kunali, atamva Yerobiamu mwana…