2 Mafumu 21

Manase woipitsitsa 1 Manase anali wa zaka khumi ndi ziwiri polowa iye ufumu wace, nakhala mfumu zaka makumi asanu ndi zisanu m’Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Hefisiba. 2 Ndipo…

2 Mafumu 22

Yosiya wabwino akonzanso kacisi 1 Yosiya ndiye wa zaka zisanu ndi zitatu polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka makumi atatu mphambu cimodzi m’Yerusalemu; ndi dzina la mace ndi Yedida mwana…

2 Mafumu 23

Yosiya awerenga bukulo kwa anthu nacita pangano ndi Yehova, nakonza zoipsa zambiri 1 Pamenepo mfumu inatumiza anthu, namsonkhanitsira akulu onse a Yuda ndi a m’Yerusalemu. 2 Nikwera mfumu kumka ku…

2 Mafumu 24

1 Masiku ace Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anakwerako, Yoyakimu nagwira mwendo wace zaka zitatu; pamenepo anatembenuka nampandukira. 2 Ndipo Yehova anamtumizira magulu a Akasidi, ndi magulu a Aaramu, ndi…

2 Mafumu 25

Yerusalemu apasulidwa, anthu natengedwa kunka ku Babulo 1 Ndipo kunali caka cacisanu ndi cinai ca ufumu wace, mwezi wakhumi, tsiku lakhumi la mwezi, Nebukadinezara mfumu ya Babulo, iye ndi khamu…