2 Mafumu 11

A taliya aononga mbumba yacifumu ya Yuda; apulumuka Yoasi, aphedwa Ataliya 1 Pamene Ataliya mace wa Ahaziya anaona kuti mwana wace wafa, ananyamuka, naononga mbeu yonse yacifumu. 2 Koma Yoseba…

2 Mafumu 12

Yoasi akonza Kacisi 1 Caka cacisanu ndi ciwiri ca Yehu, Yoasi analowa ufumu wace; nakhala mfumu m’Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la mai wace ndiye Zibiya wa ku Beereseba….

2 Mafumu 13

Yoahazi mfumu ya Israyeli 1 Caka ca makumi awiri ndi zitatu ca Yoasi mwana wa Ahaziya mfumu ya Yuda, Yoahazimwana wa Yehu analowa ufumu wace wa Israyeli ku Samariya, nakhala…

2 Mafumu 14

Amaziyamfumu ya Yuda, Yoasi ndi Yerobiamu waciwiri mafumu a Israyeli 1 Caka caciwiri ca Yoasi mwana wa Yoahazi mfumu ya Israyeli, Amaziya mwana wa Yoasi mfumu ya Yuda analowa ufumu…

2 Mafumu 15

Azariya mfumu ya Yuda 1 Caka ca makumi awiri mphambu zisanu ndi ziwiri ca Yerobiamu mfumu ya Israyeli, Azariya mwana wa Amaziya mfumu ya Yuda analowa ufumu wace. 2 Anali…

2 Mafumu 16

Ahazi mfumu ya Yuda 1 Caka cakhumi mphambu zisanu ndi ziwiri ca Peka mwana wa Remaliya Ahazi mwana wa Yotamu mfumu ya Yuda analowa ufumu wace. 2 Ahazi anali wa…

2 Mafumu 17

Hoseyamfumu yotsiriza ya Israyeli, Salimanezeri mfumu ya Asuri apasula Samariya, Aisrayeli natengedwa ukapolo 1 Caka cakhumi ndi ziwiri ca Ahazi mfumu ya Yuda Hoseya mwana wa Ela analowa ufumu wace…

2 Mafumu 18

Hezekiya wabwino akhazikanso cipembedzo ca Yehova 1 Ndipo kunali caka cacitatu ca Hoseya mwana wa Ela mfumu ya Israyeli, Hezekiya mwana wa Ahazi mfumu ya Yuda analowa ufumu waceo 2…

2 Mafumu 19

Nkhawa ya Hezekiya ndi pemphero lace 1 Ndipo kunali, atamva Hezekiya, anang’amba zobvala zace, napfundira ciguduli, nalowa m’nyumba ya Yehova. 2 Natuma Eliyakimu woyang’anira nyumbayo, ndi Sebina mlembi, ndi akuru…

2 Mafumu 20

Hezekiya adwala nacira 1 Masiku ajawo Hezekiya anadwala, nafuna kufa. Namdzera Yesaya mneneri mwana wa Amozi, nanena naye, Atero Yehova, Siyira banja lako; pakuti udzafa, sudzakhala ndi moyo. 2 Pamenepo…