2 Atesalonika 1

1 PAULO, ndi Silvano, ndi Timoteo, kwa Mpingo wa Atesalonika mwa Mulungu Atate wathu ndi Ambuye Yesu Kristu: 2 Cisomo kwa inu ndi mtendere wa kwa Mulungu Atate ndi Ambuye…

2 Atesalonika 2

Asanabwere Kristu adzaoneka wokana Kristu 1 Ndipo tikupemphani, abale, cifukwa ca kudza kwace kwa Ambuye wathu Yesu Kristu, ndi kusonkhana pamodzi kwathu kwa iye; 2 kuti musamagwedezeka mtima msanga ndi…

2 Atesalonika 3

Zowacenieza ndi malankhulano 1 Cotsalira, abale, mutipempherere, kuti mau a Ambuye athamange, nalemekezedwe, monganso kwanu; 2 ndi kuti tilanditsidwe m’manja a anthu osayenerandi oipa; pakuti si onse ali naco cikhulupiriro….