2 Akorinto 11

Za atumwi onyenga 1 Mwenzi mutandilola pang’ono ndi copusaco! Komanso mundilole. 2 Pakuti ndicita nsanje pa inu ndi nsanje ya Mulungu; pakuti ndinakupalitsani ubwenzi mwamuna mmodzi, kuti ndikalangize inu ngati…

2 Akorinto 12

Masomphenya a Paulo ndi munga m’thupi lace 1 Ndiyenera kudzitamandira, kungakhale sikupindulika; koma ndidzadza ku masomphenya ndi mabvumbulutso a Ambuye. 2 Ndidziwa munthu wa mwa Kristu, zitapita zaka khumi ndi…

2 Akorinto 13

1 Nthawi yacitatu iyi ndirinkudza kwa inu. Pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu maneno onse adzakhazikika. 2 Ndinanena kale, ndipo ndinena ndisanafikeko, monga pamene ndinali pomwepo kaciwiri kaja, pokhala ine…