2 Akorinto 1

1 PAULO, mtumwi wa Kristu Yesu, mwa cifuniro ca Mulungu, ndi Timoteo mbaleyo, kwa Mpingo wa Mulungu umene uli ku Korinto, pamodzi ndi oyera mtima onse amene ali m’Akaya lonse:…

2 Akorinto 2

1 Koma ndinatsimikiza mtima mwa ine ndekha, ndisadzenso kwa inu ndi cisoni. 2 Pakuti ngati ine ndimvetsa inu cisoni, ndaninso amene adzandikondweretsa ine, kama iye amene ndammvetsa cisoni? 3 Ndipo…

2 Akorinto 3

1 Kodi tirikuyambanso kudzibvomereza tokha? kapena kodi tisowa, monga ena, akalata otibvomerezetsa kwa inu, kapena ocokera kwa inu? 2 Inu ndinu kalata wathu, wolembedwa mu mitima yathu, wodziwika ndi wowerengedwa…

2 Akorinto 4

Paulo alalikira Yesu yekha yekha 1 Cifukwa cace popeza tiri nao utumiki umene, monga talandira cifundo, sitifoka; 2 koma takaniza zobisfka za manyazi, osayendayenda mocenjerera, kapena kucita nao mau a…

2 Akorinto 5

1 Pakuti tidziwa kuti ngati nyumba ya pansi pano ya msasa wathu ipasuka, tiri naco cimango ca kwa Mulungu, ndiyo nyumba yosamangidwa ndi manja, yosatha, m’Mwamba. 2 Pakutinso m’menemo tibuula,…

2 Akorinto 6

Kudzikana kwa Paulo m’utumiki wace 1 Ndipo a ocita naye pamodzi tidandauliranso kuti musalandire cisomo ca Mulungu kwacabe inu, 2 (pakuti anena, M’nyengo yolandiridwa ndinamva iwe, Ndipo m’tsiku la cipulumutso…

2 Akorinto 7

Paulo akondwerapa kudza kwa Tito, ndi pa zipatso za kalata wace woyamba 1 Pokhala nao tsono malonjezano amenewa, okondedwa, tidzikonzere tokha kuleka codetsa conse ca thupi ndi ca mzimu, ndi…

2 Akorinto 8

Cipereko ca kwa Akristu aumphawi a ku Yerusalemu 1 Ndipo tikudziwitsani, abale, cisomo ca Mulungu copatsika mwa Mipingo ya ku Makedoniya, 2 kuti m’citsimikizo cacikuru ca cisautso, kucurukitsa kwa cimwemwe…

2 Akorinto 9

1 Pakutitu za utumiki wa kwa oyera mtima sikufunika kwa ine kulembera inu; 2 pakuti ndidziwa cibvomerezo canu cimene ndidzitamandira naco cifukwa ca inu ndi Amakedoniya, kuti Akaya anakonzekeratu citapita…

2 Akorinto 10

Ulamuliro wa Paulo mtumwi 1 Koma ine ndekha Paulo, ndidandaulira inu mwa kufatsa ndi ulere wa Kristu, ine amene pamaso panu ndikhala wodzicepetsa pakati pa inu, koma pokhala kwina ine…