1 Timoteo 1

Paulo alangiza Timoteo 1 PAULO, mtumwi wa Kristu Yesu monga mwa cilamuliro ca Mulungu Mpulumutsi wathu, ndi ca Kristu Yesu, ciyembekezo cathu: 2 kwa Timoteo mwana wanga weniweni m’cikhulupiriro: Cisomo,…

1 Timoteo 2

Pempherero la kwa anthu onset 1 Ndidandaulira tsono, poyambayamba, kuti acitike mapembedzo, mapemphero, mapembedzero, mayamiko, cifukwa ca anthu onse; 2 cifukwa ca mafumu ndi onse akucita ulamuliro kuti m’moyo mwathu…

1 Timoteo 3

Zoyenera oyang’anira ndi atumiki 1 Mauwa ali okhulupirika, ngati munthu akhumba udindo wa woyang’anira, aifuna nchito yabwino. 2 Ndipo kuyenera woyang’anira akhale wopanda cirema, mwamuna wa mkazi mmodzi, wodzisunga, wodziletsa,…

1 Timoteo 4

Cipanduko ca m’masiku otsiriza 1 Koma Mzimu anena monenetsa, kuti m’masiku otsiriza ena adzataya cikhulupiriro, ndi kusamala mizimu yosoceretsa ndi maphunziro a ziwanda, 2 m’maonekedwe onyenga a iwo onena mabodza,…

1 Timoteo 5

Za okalamba ndi amasiye 1 Mkulu usamdzudzule, komatu umdandaulire ngati atate; anyamata ngati abale; 2 akazi akulu ngati amai; akazi ang’ono ngati alongo, m’kuyera mtima konse. 3 Citira ulemu amasiye…

1 Timoteo 6

Zoyenera akapolo 1 Onse amene ali akapolo a m’goli, ayesere ambuye a iwo okha oyenera ulemu wonse, kuti dzina la Mulungu ndi ciphunzitso zisacitidwe mwano. 2 Ndipo iwo akukhala nao…