1 Samueli 11

Sauli alanditsa Yabezi Gileadi m’manja mwa Aamoni 1 Pamenepo Nahasi M-amoni anakwera, namanga Yabezi Gileadi zithando; ndipo anthu onse a ku Yabezi anati kwa Nahasi, Mupangane cipangano ndi ife, ndipo…

1 Samueli 12

Samueli adzinenera kwa anthu 1 Ndipo Samueli anauza Aisrayeli onse, kuti, Onani dani ndinamvera mau anu mwa zonse munalankhula ndi ine, ndipo ndinakulongerani mfumu. 2 Ndipo tsopano, siyi mfumu idzayendabe…

1 Samueli 13

Nkhondo pakati pa Israyeli ndi Afilisti 1 Sauli anali ndi zaka makumi atatu pamene anayamba ufumu wace; nakhala mfumu ya Israyeli zaka ziwiri. 2 Pamenepo Sauli anadzisankhira anthu zikwi zitatu…

1 Samueli 14

Jonatani agonjetsa Afilisti 1 Ndipo kunali tsiku lina kuti Jonatani mwana wa Sauli ananena ndi mnyamata wonyamula zida zace, Tiye tipite kunka ku kaboma ka Afilisti, tsidya lija. Koma sanauza…

1 Samueli 15

Sauli alamulidwa aononge Amaleki 1 Ndipo Samueli ananena ndi Sauli, Yehova ananditumiza ine kukudzozani mukhale mfumu ya anthu ace Aisrayeli; cifukwa cace tsono mumvere kunena kwa mau a Yehova. 2…

1 Samueli 16

Samueli adzoza Davide akhale mfumu 1 Ndipo Yehova ananena ndi Samueli, Iwe ukuti ulire cifukwa ca Sauli nthawi yotani, popeza Ine ndinamkana kuti asakhale mfumu ya Israyeli? Dzaza nyanga yako…

1 Samueli 17

Davide apha Goliati 1 Pamenepo Afilisti anasonkhanitsa makamu ao a nkhondo, naunjikana ku Soko wa ku Yuda, namanga zithando pakati pa Soko ndi Azeka ku Efesi-damimu. 2 Ndipo Sauli ndi…

1 Samueli 18

Ubwenzi wa Davide ndi Jonatani 1 Ndipo kunali, pakutsiriza iye kulankhula ndi Sauli, mtima wa Jonatani unalumikizika ndi mtima wa Davide, ndipo Jonatani anamkonda iye monga moyo wa iye yekha….

1 Samueli 19

Jonatani anenera Davide kwa Sauli 1 Ndipo Sauli analankhula kwa Jonatani mwana wace, ndi anyamata ace onse kuti amuphe Davide. 2 Koma Jonatani mwana wa Sauli anakondwera kwambiri ndi Davide….

1 Samueli 20

Pangano pakati pa Davide ndi Jonatani 1 Ndipo Davide anathawa ku Nayoti m’Rama, nadzanena pamaso pa Jonatani, Ndacitanji ine? kuipa kwanga kuli kotani? ndi chimo langa la pamaso pa atate…