1 Samueli 1

1 NDIPO panali munthu wina wa ku Ramatayimu Zofimu, wa dziko la mapiri la Efraimu, dzina lace ndiye Elikana, mwana wace wa Yerohamu, mwana wa Elihu, mwana wa Tohu, mwana…

1 Samueli 2

Coyamikira ca Hana 1 Ndipo Hana anapemphera, nati Mtima wanga umyuka mokondwera kwa Yehova, Nyanga yanga yakwezeka mwa Yehova; Pakamwa panga pakula kwa adani anga; Popeza ndikondwera m’cipulumutsocanu. 2 Palibe…

1 Samueli 3

Masomphenya a Samueli 1 Ndipo mwanayo Samueli anatumikira Yehova pamaso pa Eli. Ndipo masiku aja mau a Yehova anamveka kamodzi kamodzi; masomphenya sanaoneka-oneka. 2 Ndipo kunali nthawi yomweyo Eli atagona…

1 Samueli 4

Afilisti akantha Aisrayeli 1 Ndipo mau a Samueli anafikira kwa Aisrayeli onse. Ndipo Aisrayeli anaturuka kukaponyana nkhondo ndi Afilisti, namanga zithando zao ku Ebenezeri; Afilistiwo namanga m’Afeki. 2 Ndipo Afilistiwo…

1 Samueli 5

Likasa la Mulungu ku nyumba ya Dagoni 1 Ndipo Afilisti anatenga likasa la Mulungu, nacoka nalo ku Ebenezeri, napita ku Asidodi. 2 Ndipo Afilistiwo anatenga likasa la Mulungu, nafika nalo…

1 Samueli 6

Afilisti abweza likasa ku dziko la Aisrayeli 1 Ndipo likasa la Yehova linakhala ku dziko la Afilisti miyezi isanu ndi iwiri. 2 Ndipo Afilistiwo anaitana ansembe ndi oombeza, nati, Ticitenji…

1 Samueli 7

1 Ndipo anthu a ku Kiriati-yearimu anabwera, natenga likasa la Yehova, nafika nalo m’nyumba ya Abinadabu paphiri; napatula mwana wace wamwamuna Eleazeri kuti asunge likasa la Yehova. Afilisti akanthidwa ku…

1 Samueli 8

Aisrayeli akhumba mfumu 1 Ndipo kunali, pamene Samueli anakalamba, anaika ana ace amuna akhale oweruza a Israyeli. 2 Dzina la mwana wace woyamba ndiye Yoeli, ndi dzina la waciwiri ndiye…

1 Samueli 9

Sauli afuna aburu olowerera a atate wace 1 Ndipo panali munthu Mbenlamlni, dzina lace ndiye Kisi, mwana wa Abiyeli, mwana wa Zerori, mwana wa Bekorati, mwana wa Afiya, mwana wa…

1 Samueli 10

Samueli; adzoza Sauli akhale mfumu ya Israyeli 1 Pamenepo Samueli anatenga nsupa ya mafuta, nawatsanulira pamutu pace, nampsompsona iye, nati, Sanakudzozani ndi Mulungu kodi, mukhale mfumu ya pa colowa cace?…