1 Mafumu 21

Yezebeli aphetsa Naboti 1 Ndipo zitatha izi, kunaoneka zotere: Naboti wa ku Yezreeli anali ndi munda wamphesa, unali m’Yezreelimo, m’mbali mwa nyumba ya Ahabu mfumu ya ku Samaria. 2 Ndipo…

1 Mafumu 22

Ahabu apangana ndi Yehosafati 1 Ndipo Aaramu ndi Aisrayeli anakhala cete zaka zitatu, osathirana nkhondo. 2 Koma kunacitika caka cacitatu, kuti Yehosafati mfumu ya Yuda anatsikira kwa mfumu ya Israyeli….