1 Mafumu 1
Ukalamba wa Davide, achula Saloma wodzalowa m’malo mwace 1 NDIPO mfumu Davide anakalamba nacuruka masiku ace; ndipo iwo anampfunda ndi zopfunda, koma iye sanafundidwa. 2 Pamenepo anyamata ace ananena naye,…
Ukalamba wa Davide, achula Saloma wodzalowa m’malo mwace 1 NDIPO mfumu Davide anakalamba nacuruka masiku ace; ndipo iwo anampfunda ndi zopfunda, koma iye sanafundidwa. 2 Pamenepo anyamata ace ananena naye,…
Davide atapangira Solomo amwalira 1 Pakuyandikira masiku ace a Davide akuti amwalire, analamulira Solomo mwana wace, nati, 2 Ndimuka ine njira ya dziko lonse: limba mtima tsono, nudzionetse umunthu; 3…
Solomo akwatira mwana wa Farao 1 Ndipo Solomo anapalana ubwenzi ndi Farao mfumu ya Aigupto, natenga mwana wamkazi wa Farao, nadza naye ku mudzi wa Davide, mpaka atamanga nyumba ya…
Nduna za Solomo, ukuru wa ufumu wace 1 Ndipo mfumu Solomo anali mfumu ya Israyeli yense. 2 Ndipo akuru a mfumu ndi awa: Azariya mwana wa Zadoki anali nduna, 3…
Solomo apangana ndi Hiramu za mirimo vomansa nayo Kacisi 1 Ndipo Hiramu mfumu ya ku Turo anatuma anyamata ace kwa Solomo, popeza anamva kuti adamdzoza mfumu m’malo mwa atate wace;…
Za mamangidwe a Kacisi 1 Ndipo kunacitika zitapita zaka mazana anai mphambu makumi asanu ndi atatu ataturuka ana a Israyeli m’dziko la Aigupto, caka cacinai cakukhala Solomo mfumu ya Israyeli,…
Mamangidwe a nyumba Yd Solomo 1 Koma nyumba ya iye yekha Solomo anaimanga zaka khumi mphambu zitatu, natsiriza nyumba yace yonse. 2 Anamanganso nyumba yochedwa Nkhalango ya Lebano, m’litali mwace…
Aika likasa m’Kacisi 1 Pamenepo Solomo anasonkhanitsa akulu a Israyeli, ndi akulu onse a mafuko, akalonga a nyumba za atate a ana a Israyeli, kwa mfumu Solomo m’Yerusalemu, kukatenga likasa…
Mulungu aonekanso kwa Solomo 1 Ndipo kunali, atatsiriza Solomo kumanga nyumba ya Yehova, ndi nyumba ya mfumu, ndi cifuniro conse ca Solomo anacikhumbaco, 2 Yehova anaonekera kwa Solomo nthawi yaciwiri,…
Mfumu yaikazi ya ku Seba adzaceza kwa Solomo ku Yerusalemu 1 Ndipo atamva mfumu yaikazi ya ku Seba mbiri ya Solomo yakubukitsa dzina la Yehova, anadza kumuyesera iye ndi miyambi…