1 Atesalonika 1

1 PAULO, ndi Silvano, ndi Timoteo, kwa Mpingo wa Atesalonika mwa Mulungu Atate ndi Ambuye Yesu Kristu: Cisomo kwa inu ndi mtendere. Zipatso za Uthenga Wabwino ku Tesalonika 2 Tiyamika…

1 Atesalonika 2

Za utumiki wace wa kwa Atesalonika 1 Pakuti, abale, mudziwa nokha malowedwe athu a kwa inu, kuti sanakhala opanda pace; 2 koma tingakhale tidamva zowawa kale, ndipo anaticitira cipongwe, monga…

1 Atesalonika 3

1 Cifukwa cace, posakhoza kulekereranso, tidabvomereza mtima atisiye tokhaku Atene; 2 ndipo tinatuma Timoteo, mbale wathuyo ndi mtumiki wa Mulungu m’Uthenga Wabwino wa Kristu, kuti akhazikitse inu; ndi kutonthoza inu…

1 Atesalonika 4

Atsate kuyera-mtima, cikondano, ndi khama 1 Cotsalira tsono, abale, tikupemphani ndi kukudandaulirani mwa Ambuye Yesu, kuti, monga munalandira kwa ife mayendedwe okoma, muyenera kuyendanso ndi kukondweretsa Mulungu, monganso mumayenda, eurukani…

1 Atesalonika 5

1 Koma za nthawizo ndi nyengozo, abale, sikufunika kuti tidzakulemberani, 2 Pakuti inu nokha mudziwa bwino kuti tsiku la Ambuye lidzadza monga mbala usiku, 3 Pamene angonena, Mtendere ndi mosatekeseka,…