1 Akorinto 11

1 Khalani onditsanza ine, monga inenso oditsanza Kristu. Za akazi m’Eklesia wa Ambuye 2 Ndipo ndikutamandani kuti m’zinthu zonse mukumbukila ine, ndi kuti musunga miyambo monga ndinapereka kwa inu. 3…

1 Akorinto 12

Mphatso ta Mzimu zisiyana 1 Koma za mphatso zauzimu, abale, sindifuna kuti mukhale osadziwa. 2 Mudziwa kuti pamene munali amitundu, munatengedwa kunka kwa mafano aja osalankhula, monga munatsogozedwa. 3 Cifukwa…

1 Akorinto 13

Kuposa kwa Cikondi 1 Ndingakhale ndilankhula malilime a anthu, ndi a angelo, koma ndiribe cikondi, ndikhala mkuwa woomba, kapena nguli yolira. 2 Ndipo ndingakhale ndikhoza kunenera, ndipo ndingadziwe zinsinsi zonse,…

1 Akorinto 14

Mpnatso ya kunenera tposa ya malilime 1 Tsatani cikondi; koma funitsitsani mphatsozauzimu, koma koposa kuti mukanenere. 2 Pakuti iye wakulankhula lilime salankhula ndi anthu, koma ndi Mulungu; pakuti palibemunthu akumva;…

1 Akorinto 15

Za kuuka kwa akufa 1 Ndipo ndikudziwitsani, abale, Uthenga Wabwino umene ndinakulalikirani inu, umenenso munalandira, umenenso muimamo, 2 umenenso mupulumutsidwa nao ngati muugwiritsa monga momwe ndinalalikira kwa inu; ngati simunakhulupira…

1 Akorinto 16

Zopereka za kwa Akristu a ku Yerusalemu 1 Koma za copereka ca kwa oyera mtima, mongandinalangiza Mipingo ya ku Galatiya, motero citani inunso. 2 Tsiku loyamba la sabata yense wa…