1 Akorinto 1

1 PAULO, woitanidwa akhale mtumwi wa Yesu Kristu mwa cifuniro ca Mulungu, ndi Sositene mbaleyo, 2 kwa Mpingo wa Mulungu wakukhala m’Korinto, ndiwo oyeretsedwa mwa Kristu Yesu, oitanidwa akhale oyera…

1 Akorinto 2

Ulalikidwe wa Paulo 1 Ndipo ine, abale, m’mene ndinadza kwa inu, sindinadza ndi kuposa kwa mau, kapena kwa nzeru, polalikira kwa inu cinsinsi ca Mulungu. 2 Pakuti ndinatsimikiza mtima kuti…

1 Akorinto 3

Cifukwa ca malekano ao 1 Ndipo ine, abale, sindinakhoza kulankhula ndi inu manga ndi auzimu, koma monga athupi, monga makanda mwa Kristu. 2 Ndinaiyetsa inu mkaka, si cakudya colimba ai;…

1 Akorinto 4

Atumiki a Kristu ndi ogawira zinsinsi za Mulungu 1 Cotero munthu atiyese ife, monga atumiki a Kristu, ndi adindo a zinsinsi za Mulungu. 2 Komatu pano pafunika za adindo, kuti…

1 Akorinto 5

Za cigololo mu Mpingo wa ku Korinto, Awadzudzulapo 1 Kwamveka ndithu kuti kuli cigololo pakati pa inu, ndipo cigololo cotere conga sicimveka mwa amitundu, kuti wina ali naye mkazi wa…

1 Akorinto 6

Awadzudzula pa mirandu ya pakati pa abale 1 Kodiakhoza winawa inu, pamene ali nao mlandu pa mnzace, kupita kukaweruzidwa kwa osalungama, osati kwa oyera mtima? 2 Kapena kodi simudziwa kuti…

1 Akorinto 7

Mau a za ukwati 1 Koma za izi munalembazi; kuli bwino kwa munthu kusakhudza mkazi. 2 Koma cifukwa ca madama munthu yense akhale naye mkazi wa iye yekha, ndi mkazi…

1 Akorinto 8

Kunena za kudya nyama yoperekedwa nsembe kwa mafano 1 Koma za zoperekedwa nsembe kwa mafano: Tidziwa kuti tid naco cidziwitso tonse. Cidziwitso citukumula, koma cikondicimangirira. 2 Ngati wina ayesa kuti…

1 Akorinto 9

Ululu ndi ulamuliro wa mtumwiyo 1 Kodi sindine mfulu? Kodi slndine mtumwi? Kodi sindinaona Yesu Ambuye wathu? Kodi simuli inu nchito yanga mwa Ambuye? 2 Ngati sindiri mtumwi kwa ena,…

1 Akorinto 10

Tisayese dala Mulungu monga Israyeli 1 Pakuti sindifuna, kuti mukhale osadziwa, abale, kuti makolo athu onse anali pansi pa mtambo, naoloka nyanja onse; 2 nabatizidwa onse kwa Mose, mumtambo, ndi…